Miyambo 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Sikelo yachinyengo imam’nyansa Yehova,+ koma mwala woyezera, wolemera mokwanira, umam’sangalatsa. Miyambo 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Miyezo iwiri yosiyana yoyezera kulemera kwa chinthu ndi yonyansa kwa Yehova,+ ndipo sikelo yachinyengo si yabwino.+ Hoseya 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 M’manja mwa wamalonda muli sikelo yachinyengo+ ndipo iye amakonda kuba mwachinyengo.+
23 Miyezo iwiri yosiyana yoyezera kulemera kwa chinthu ndi yonyansa kwa Yehova,+ ndipo sikelo yachinyengo si yabwino.+