Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 20:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Pokumbukira kuti muyenera kusunga tsiku la sabata ndi kuliona kukhala lopatulika,+

  • Nehemiya 13:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Masiku amenewo ku Yuda ndinaona anthu akuponda moponderamo mphesa tsiku la sabata.+ Anali kubweretsa mbewu ndi kuzikweza+ pa abulu.+ Analinso kukweza pa abuluwo vinyo, mphesa, nkhuyu+ ndi katundu wosiyanasiyana ndipo anali kubwera nazo ku Yerusalemu tsiku la sabata.+ Ine ndinawadzudzula pa tsiku limene anali kugulitsa zinthu zimenezi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena