Ekisodo 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo iye anawayankha kuti: “Ndi zimene Yehova wanena. Mawa tisunga sabata, sabata lopatulika la Yehova.+ Zimene mungaphike, phikani, ndipo zimene mungawiritse, wiritsani.+ Zotsala zonse muziike pambali ndi kuzisunga mpaka m’mawa.” Ekisodo 31:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Koma iwe uuze ana a Isiraeli kuti, ‘Muonetsetse kuti muzisunga masiku anga a sabata,+ pakuti ndi chizindikiro pakati pa ine ndi inu m’mibadwo yanu yonse, kuti mudziwe kuti ine Yehova ndakusankhani kukhala opatulika.+ Deuteronomo 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “‘Posunga tsiku la sabata ndi kuliona kukhala lopatulika, mmene Yehova Mulungu wako anakulamulira,+
23 Ndipo iye anawayankha kuti: “Ndi zimene Yehova wanena. Mawa tisunga sabata, sabata lopatulika la Yehova.+ Zimene mungaphike, phikani, ndipo zimene mungawiritse, wiritsani.+ Zotsala zonse muziike pambali ndi kuzisunga mpaka m’mawa.”
13 “Koma iwe uuze ana a Isiraeli kuti, ‘Muonetsetse kuti muzisunga masiku anga a sabata,+ pakuti ndi chizindikiro pakati pa ine ndi inu m’mibadwo yanu yonse, kuti mudziwe kuti ine Yehova ndakusankhani kukhala opatulika.+
12 “‘Posunga tsiku la sabata ndi kuliona kukhala lopatulika, mmene Yehova Mulungu wako anakulamulira,+