Salimo 42:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Monga mmene mbawala yaikazi imalakalakira mitsinje ya madzi,Moyo wanganso ukulakalaka inu Mulungu wanga.+ Salimo 119:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Ndidzapemphera kwa inu nditakweza manja anga chifukwa ndimakonda malamulo anu,+Ndipo ndidzasinkhasinkha malangizo anu.+
42 Monga mmene mbawala yaikazi imalakalakira mitsinje ya madzi,Moyo wanganso ukulakalaka inu Mulungu wanga.+
48 Ndidzapemphera kwa inu nditakweza manja anga chifukwa ndimakonda malamulo anu,+Ndipo ndidzasinkhasinkha malangizo anu.+