Danieli 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu ambiri adzadzitsuka,+ adzadziyeretsa+ ndipo adzayengedwa.+ Anthu oipa adzachita zinthu zoipa+ ndipo palibe munthu woipa aliyense amene adzamvetsetse mawu amenewa,+ koma anthu ozindikira adzawamvetsetsa.+ Mateyu 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Odala ndi anthu oyera mtima,+ chifukwa adzaona Mulungu.+
10 Anthu ambiri adzadzitsuka,+ adzadziyeretsa+ ndipo adzayengedwa.+ Anthu oipa adzachita zinthu zoipa+ ndipo palibe munthu woipa aliyense amene adzamvetsetse mawu amenewa,+ koma anthu ozindikira adzawamvetsetsa.+