Salimo 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zingwe za imfa zinandikulunga,+Chikhamu cha anthu opanda pake chinali kundiopseza.+ Salimo 88:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ine ndakumana ndi masoka ochuluka,+Ndipo moyo wanga wayandikira ku Manda.+ Maliko 14:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndiyeno anawauza kuti: “Moyo wanga ukumva chisoni chofa nacho.+ Khalani pompano ndipo mukhalebe maso.”+
34 Ndiyeno anawauza kuti: “Moyo wanga ukumva chisoni chofa nacho.+ Khalani pompano ndipo mukhalebe maso.”+