Salimo 140:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Muwakhuthulire makala oyaka moto pamutu pawo.+Muwachititse kugwera m’moto+ ndi m’madzi akuya kuti asanyamukenso.+ Miyambo 16:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Munthu wopanda pake amafukula zinthu zoipa,+ ndipo pakamwa pake pamakhala mawu okhala ngati makala amoto.+
10 Muwakhuthulire makala oyaka moto pamutu pawo.+Muwachititse kugwera m’moto+ ndi m’madzi akuya kuti asanyamukenso.+
27 Munthu wopanda pake amafukula zinthu zoipa,+ ndipo pakamwa pake pamakhala mawu okhala ngati makala amoto.+