Salimo 113:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Dzina la Yehova lidalitsike,+Kuyambira tsopano mpaka kalekale.+ Salimo 115:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma ife tidzatamanda Ya+Kuyambira tsopano mpaka kalekale.+Tamandani Ya, anthu inu!+