Genesis 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo Sarai mkazi wa Abulamu anapereka Hagara, kapolo wake Mwiguputo, kwa mwamuna wake Abulamu kuti akhale mkazi wake.+ Zimenezi zinachitika Abulamu atakhala zaka 10 m’dziko la Kanani.
3 Pamenepo Sarai mkazi wa Abulamu anapereka Hagara, kapolo wake Mwiguputo, kwa mwamuna wake Abulamu kuti akhale mkazi wake.+ Zimenezi zinachitika Abulamu atakhala zaka 10 m’dziko la Kanani.