Genesis 49:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndithu ndidzayembekezera chipulumutso kwa inu, Yehova.+ Salimo 119:82 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 82 Maso anga alefuka chifukwa cholakalaka mawu anu,+Ndipo ndikunena kuti: “Kodi mudzandilimbikitsa liti?”+ Salimo 119:123 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 123 Maso anga afooka chifukwa cholakalaka chipulumutso chanu+Ndi mawu anu olungama.+ Salimo 130:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndayembekezera Yehova+Kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche,+Ndithu kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche.+
82 Maso anga alefuka chifukwa cholakalaka mawu anu,+Ndipo ndikunena kuti: “Kodi mudzandilimbikitsa liti?”+
6 Ndayembekezera Yehova+Kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche,+Ndithu kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche.+