Salimo 119:123 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 123 Maso anga afooka chifukwa choyembekezera chipulumutso chanu+Komanso malonjezo* anu olungama.+