Aroma 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komanso Malemba amati: “Kondwerani, mitundu inu, pamodzi ndi anthu ake.”+ Chivumbulutso 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi ndani sadzakuopani,+ inu Yehova?+ Ndani sadzalemekeza dzina lanu?+ Pakuti inu nokha ndinu wokhulupirika.+ Mitundu yonse ya anthu idzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa malamulo anu olungama aonekera.”+
4 Kodi ndani sadzakuopani,+ inu Yehova?+ Ndani sadzalemekeza dzina lanu?+ Pakuti inu nokha ndinu wokhulupirika.+ Mitundu yonse ya anthu idzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa malamulo anu olungama aonekera.”+