Salimo 78:70 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 Choncho anasankha Davide mtumiki wake,+Ndipo anamuchotsa kumakola a nkhosa.+ Yeremiya 45:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma iwe, ukufunafunabe zinthu zazikulu.+ Leka kuzifunafuna.”’+ “‘Anthu onse ndikuwagwetsera tsoka+ ndipo iwe ndidzakupatsa moyo wako monga chofunkha chako kulikonse kumene ungapite,’ watero Yehova.”+ Amosi 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo Amosi anayankha Amaziya kuti: “Ine sindinali mneneri kapena mwana wa mneneri,+ koma ndinali m’busa+ ndiponso woboola nkhuyu. Aroma 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muziona ena mmene inuyo mumadzionera.+ Musamaganize modzikweza,+ koma khalani ndi mtima wodzichepetsa.+ Musadziyese anzeru.+
5 Koma iwe, ukufunafunabe zinthu zazikulu.+ Leka kuzifunafuna.”’+ “‘Anthu onse ndikuwagwetsera tsoka+ ndipo iwe ndidzakupatsa moyo wako monga chofunkha chako kulikonse kumene ungapite,’ watero Yehova.”+
14 Pamenepo Amosi anayankha Amaziya kuti: “Ine sindinali mneneri kapena mwana wa mneneri,+ koma ndinali m’busa+ ndiponso woboola nkhuyu.
16 Muziona ena mmene inuyo mumadzionera.+ Musamaganize modzikweza,+ koma khalani ndi mtima wodzichepetsa.+ Musadziyese anzeru.+