2 Samueli 22:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndidzawawononga onse ndi kuwaphwanya zibenthuzibenthu+ kuti asadzukenso.+Iwo adzagwa pansi ndipo ndidzawapondaponda ndi mapazi anga.+ Salimo 110:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Adzapereka chiweruzo pakati pa anthu a mitundu ina.+Adzachititsa mitembo ya anthu kupezeka paliponse.+Adzaphwanyaphwanya mtsogoleri wa dziko la anthu ambiri.+
39 Ndidzawawononga onse ndi kuwaphwanya zibenthuzibenthu+ kuti asadzukenso.+Iwo adzagwa pansi ndipo ndidzawapondaponda ndi mapazi anga.+
6 Adzapereka chiweruzo pakati pa anthu a mitundu ina.+Adzachititsa mitembo ya anthu kupezeka paliponse.+Adzaphwanyaphwanya mtsogoleri wa dziko la anthu ambiri.+