2 Mafumu 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye anapitiriza kuyenda m’njira zonse zimene bambo ake anayendamo,+ ndipo anapitiriza kutumikira mafano onyansa+ amene bambo ake anawatumikira, n’kumawagwadira. Salimo 97:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Onse amene akupembedza chifaniziro chilichonse achite manyazi.+Amene amadzitama chifukwa cha milungu yopanda pake achite manyazi.+Muweramireni, inu milungu yonse.+
21 Iye anapitiriza kuyenda m’njira zonse zimene bambo ake anayendamo,+ ndipo anapitiriza kutumikira mafano onyansa+ amene bambo ake anawatumikira, n’kumawagwadira.
7 Onse amene akupembedza chifaniziro chilichonse achite manyazi.+Amene amadzitama chifukwa cha milungu yopanda pake achite manyazi.+Muweramireni, inu milungu yonse.+