Genesis 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Mulungu anati: “Kukhale zounikira kuthambo kuti zilekanitse usana ndi usiku+ ndipo zikhale zizindikiro, komanso kuti zisonyeze nyengo ndi masiku ndi zaka.+ Salimo 74:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Usana ndi wanu, usikunso ndi wanu.+Inu munapanga chounikira, munapanga dzuwa.+
14 Kenako Mulungu anati: “Kukhale zounikira kuthambo kuti zilekanitse usana ndi usiku+ ndipo zikhale zizindikiro, komanso kuti zisonyeze nyengo ndi masiku ndi zaka.+