Genesis 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Mulungu anati:+ “Pakhale kuwala.” Ndipo kuwala kunakhalapo.+ Genesis 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Mulungu anatcha kuwalako Usana,+ koma mdimawo anautcha Usiku.+ Panali madzulo ndiponso panali m’mawa, tsiku loyamba. Salimo 136:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yamikani wopanga zounikira zazikulu:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
5 Ndiyeno Mulungu anatcha kuwalako Usana,+ koma mdimawo anautcha Usiku.+ Panali madzulo ndiponso panali m’mawa, tsiku loyamba.
7 Yamikani wopanga zounikira zazikulu:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+