Yesaya 40:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Udzu wobiriwirawo wauma. Maluwawo afota.+ Koma mawu a Mulungu wathu adzakhala mpaka kalekale.”+ 1 Petulo 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 koma mawu a Yehova amakhala kosatha.”+ “Mawu”+ amenewo ndi amene alengezedwa+ kwa inu monga uthenga wabwino.
25 koma mawu a Yehova amakhala kosatha.”+ “Mawu”+ amenewo ndi amene alengezedwa+ kwa inu monga uthenga wabwino.