1 Petulo 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 koma mawu a Yehova* adzakhalapo mpaka kalekale.”+ “Mawu” amenewa ndi uthenga wabwino umene unalengezedwa kwa inu.+ 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:25 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),9/2017, ptsa. 18-19
25 koma mawu a Yehova* adzakhalapo mpaka kalekale.”+ “Mawu” amenewa ndi uthenga wabwino umene unalengezedwa kwa inu.+