Salimo 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuchokera kumwamba, Yehova wayang’ana,+Waona ana onse a anthu.+ Salimo 94:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova amadziwa kuti maganizo a anthu ali ngati mpweya wotuluka m’mphuno.+ Ezekieli 38:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Pa tsikulo maganizo adzakubwerera mumtima mwako+ ndipo udzaganiza zochita chiwembu choipa kwambiri.+ Mateyu 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Yesu, podziwa zimene iwo anali kuganiza,+ ananena kuti: “N’chifukwa chiyani mukuganiza zinthu zoipa m’mitima mwanu?+
10 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Pa tsikulo maganizo adzakubwerera mumtima mwako+ ndipo udzaganiza zochita chiwembu choipa kwambiri.+
4 Koma Yesu, podziwa zimene iwo anali kuganiza,+ ananena kuti: “N’chifukwa chiyani mukuganiza zinthu zoipa m’mitima mwanu?+