Mateyu 12:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ana a njoka inu,+ mungalankhule bwanji zinthu zabwino, pamene muli oipa?+ Pakuti pakamwa pamalankhula zosefukira mumtima.+ Aroma 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Mmero wawo ndi manda otseguka. Iwo amalankhula ndi lilime lachinyengo.”+ “M’milomo yawo muli poizoni wa njoka.”+ Yakobo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma lilime, palibe munthu ndi mmodzi yemwe angathe kuliweta. Ndilo kanthu kamodzi kosalamulirika ndi kovulaza, kodzaza ndi poizoni wakupha.+
34 Ana a njoka inu,+ mungalankhule bwanji zinthu zabwino, pamene muli oipa?+ Pakuti pakamwa pamalankhula zosefukira mumtima.+
13 “Mmero wawo ndi manda otseguka. Iwo amalankhula ndi lilime lachinyengo.”+ “M’milomo yawo muli poizoni wa njoka.”+
8 Koma lilime, palibe munthu ndi mmodzi yemwe angathe kuliweta. Ndilo kanthu kamodzi kosalamulirika ndi kovulaza, kodzaza ndi poizoni wakupha.+