Salimo 103:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 103 Tamanda Yehova, iwe moyo wanga.+Chilichonse mkati mwanga, chitamande dzina lake loyera.+ Salimo 104:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ochimwa adzafafanizidwa padziko lapansi.+Ndipo anthu oipa sadzakhalaponso.+Tamanda Yehova, iwe moyo wanga. Tamandani Ya, anthu inu!*+
35 Ochimwa adzafafanizidwa padziko lapansi.+Ndipo anthu oipa sadzakhalaponso.+Tamanda Yehova, iwe moyo wanga. Tamandani Ya, anthu inu!*+