Salimo 118:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kuthawira kwa Yehova n’kwabwino+Kusiyana ndi kudalira munthu wochokera kufumbi.+ Yesaya 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kuti zinthu zikuyendereni bwino, musadalire munthu wochokera kufumbi amene mpweya wake uli m’mphuno mwake,+ pakuti palibe chifukwa choti mum’ganizire iyeyo.+ Yeremiya 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wanena kuti: “Wotembereredwa ndi munthu aliyense wokhulupirira mwa munthu aliyense wochokera kufumbi.+ Wotembereredwa ndi munthu amene amadalira mphamvu za dzanja la munthu,+ komanso amene mtima wake wapatuka kuchoka kwa Yehova.+
22 Kuti zinthu zikuyendereni bwino, musadalire munthu wochokera kufumbi amene mpweya wake uli m’mphuno mwake,+ pakuti palibe chifukwa choti mum’ganizire iyeyo.+
5 Yehova wanena kuti: “Wotembereredwa ndi munthu aliyense wokhulupirira mwa munthu aliyense wochokera kufumbi.+ Wotembereredwa ndi munthu amene amadalira mphamvu za dzanja la munthu,+ komanso amene mtima wake wapatuka kuchoka kwa Yehova.+