Salimo 50:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti nyama iliyonse yakutchire ndi yanga,+Ndiponso nyama zopezeka m’mapiri 1,000.+ Yesaya 43:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zilombo zakutchire zidzanditamanda.+ Mimbulu ndi nthiwatiwa+ zidzanditamanda chifukwa ndidzapereka madzi ndi mitsinje m’chipululu,+ kuti anthu anga, wosankhidwa wanga,+ amwe,
20 Zilombo zakutchire zidzanditamanda.+ Mimbulu ndi nthiwatiwa+ zidzanditamanda chifukwa ndidzapereka madzi ndi mitsinje m’chipululu,+ kuti anthu anga, wosankhidwa wanga,+ amwe,