Genesis 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo analowa pamodzi ndi nyama zakutchire zamtundu uliwonse,+ nyama zoweta zamtundu uliwonse, nyama zokwawa* pansi zamtundu uliwonse,+ zolengedwa zouluka zamtundu uliwonse,+ ndiponso mbalame zilizonse ndi zolengedwa zilizonse zamapiko.+
14 Iwo analowa pamodzi ndi nyama zakutchire zamtundu uliwonse,+ nyama zoweta zamtundu uliwonse, nyama zokwawa* pansi zamtundu uliwonse,+ zolengedwa zouluka zamtundu uliwonse,+ ndiponso mbalame zilizonse ndi zolengedwa zilizonse zamapiko.+