Salimo 40:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti masoka anandizungulira moti sindinathe kuwawerenga.+Zolakwa zanga zochuluka zinandifikira modzidzimutsa moti sindinathe kuziona mmene zinachulukira.+Zinachuluka kwambiri kuposa tsitsi la kumutu kwanga,+Ndipo ndinataya mtima.+ 1 Akorinto 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti sindikudziwa+ kanthu kalikonse konditsutsa mumtima mwanga. Koma zimenezi sizikutanthauza kuti basi ndine wolungama, koma Yehova ndiye amandifufuza.+
12 Pakuti masoka anandizungulira moti sindinathe kuwawerenga.+Zolakwa zanga zochuluka zinandifikira modzidzimutsa moti sindinathe kuziona mmene zinachulukira.+Zinachuluka kwambiri kuposa tsitsi la kumutu kwanga,+Ndipo ndinataya mtima.+
4 Pakuti sindikudziwa+ kanthu kalikonse konditsutsa mumtima mwanga. Koma zimenezi sizikutanthauza kuti basi ndine wolungama, koma Yehova ndiye amandifufuza.+