Deuteronomo 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye ndi amene muyenera kum’tamanda,+ ndipo iye ndi Mulungu wanu amene wakuchitirani zinthu zazikulu ndi zochititsa mantha, zimene mwaziona ndi maso anu.+ Salimo 65:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Inu Mulungu, anthu akukutamandani mu Ziyoni+ ndipo akhala chete pamaso panu,Iwo adzakwaniritsa malonjezo awo kwa inu.+
21 Iye ndi amene muyenera kum’tamanda,+ ndipo iye ndi Mulungu wanu amene wakuchitirani zinthu zazikulu ndi zochititsa mantha, zimene mwaziona ndi maso anu.+
65 Inu Mulungu, anthu akukutamandani mu Ziyoni+ ndipo akhala chete pamaso panu,Iwo adzakwaniritsa malonjezo awo kwa inu.+