Salimo 99:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mose ndi Aroni anali pakati pa ansembe ake,+Samueli anali pakati pa anthu amene anali kuitana pa dzina lake.+Iwo anali kuitana Yehova, ndipo iye anali kuwayankha.+ Salimo 106:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Mulungu akamva kuchonderera kwawo+Anali kuona kuvutika kwawo.+
6 Mose ndi Aroni anali pakati pa ansembe ake,+Samueli anali pakati pa anthu amene anali kuitana pa dzina lake.+Iwo anali kuitana Yehova, ndipo iye anali kuwayankha.+