Salimo 47:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti Mulungu ndi Mfumu ya dziko lonse lapansi.+Imbani nyimbo zotamanda ndi kuchita zinthu mozindikira.+ Zekariya 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova adzakhala mfumu ya dziko lonse lapansi.+ Pa tsiku limenelo, Yehova adzakhala mmodzi+ ndipo dzina lake lidzakhala limodzi.+
7 Pakuti Mulungu ndi Mfumu ya dziko lonse lapansi.+Imbani nyimbo zotamanda ndi kuchita zinthu mozindikira.+
9 Yehova adzakhala mfumu ya dziko lonse lapansi.+ Pa tsiku limenelo, Yehova adzakhala mmodzi+ ndipo dzina lake lidzakhala limodzi.+