Ezekieli 34:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Nkhosazo ndidzazidyetsera m’malo a msipu wabwino ndipo zizidzakhala m’mapiri ataliatali a ku Isiraeli.+ Kumeneko zizidzagona pansi m’malo abwino kwambiri.+ Zizidzadya msipu wobiriwira bwino m’mapiri a ku Isiraeli.” Mateyu 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma poyankha iye anati: “Malemba amati, ‘Munthu sangakhale ndi moyo ndi chakudya chokha, koma ndi mawu onse otuluka pakamwa pa Yehova.’”*+
14 Nkhosazo ndidzazidyetsera m’malo a msipu wabwino ndipo zizidzakhala m’mapiri ataliatali a ku Isiraeli.+ Kumeneko zizidzagona pansi m’malo abwino kwambiri.+ Zizidzadya msipu wobiriwira bwino m’mapiri a ku Isiraeli.”
4 Koma poyankha iye anati: “Malemba amati, ‘Munthu sangakhale ndi moyo ndi chakudya chokha, koma ndi mawu onse otuluka pakamwa pa Yehova.’”*+