Salimo 37:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Khulupirira Yehova ndipo chita zabwino.+Khala padziko lapansi, ndipo khala wokhulupirika m’zochita zako zonse.+ Salimo 62:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mukhulupirireni nthawi zonse, anthu inu.+Mukhuthulireni za mumtima mwanu.+Mulungu ndiye pothawirapo pathu.+ [Seʹlah.] Miyambo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Khulupirira Yehova ndi mtima wako wonse,+ ndipo usadalire luso lako lomvetsa zinthu.+ 1 Petulo 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho amene akuvutika mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu, aike miyoyo yawo m’manja mwa Mlengi wokhulupirika, pamene akupitiriza kuchita zabwino.+
3 Khulupirira Yehova ndipo chita zabwino.+Khala padziko lapansi, ndipo khala wokhulupirika m’zochita zako zonse.+
8 Mukhulupirireni nthawi zonse, anthu inu.+Mukhuthulireni za mumtima mwanu.+Mulungu ndiye pothawirapo pathu.+ [Seʹlah.]
19 Choncho amene akuvutika mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu, aike miyoyo yawo m’manja mwa Mlengi wokhulupirika, pamene akupitiriza kuchita zabwino.+