Salimo 114:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mapiri anadumphadumpha ngati nkhosa zamphongo,+Zitunda zinadumphadumpha ngati ana a nkhosa. Yeremiya 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndinaona mapiri ndipo anali kugwedezeka. Zitunda zonse zinali kunjenjemera.+