Salimo 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Mulungu wanga, chikhulupiriro changa chili mwa inu.+Musalole kuti ndichite manyazi.Adani anga asakondwere chifukwa cha masautso anga.+ Salimo 41:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mukatero ndidziwa kuti mwasangalala nane,Chifukwa mdani wanga sadzafuula mosangalala kuti wandipambana.+
2 Inu Mulungu wanga, chikhulupiriro changa chili mwa inu.+Musalole kuti ndichite manyazi.Adani anga asakondwere chifukwa cha masautso anga.+
11 Mukatero ndidziwa kuti mwasangalala nane,Chifukwa mdani wanga sadzafuula mosangalala kuti wandipambana.+