Ekisodo 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Mnzako ukamulanda chovala chake monga chikole,+ uzim’bwezera dzuwa likamalowa. Miyambo 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Munthu amene walonjeza kuti adzapereka ngongole ya mlendo iye akadzalephera kubweza,+ zinthu sizidzamuyendera bwino. Koma wodana ndi kugwirana chanza pochita mgwirizano sakhala ndi nkhawa.
15 Munthu amene walonjeza kuti adzapereka ngongole ya mlendo iye akadzalephera kubweza,+ zinthu sizidzamuyendera bwino. Koma wodana ndi kugwirana chanza pochita mgwirizano sakhala ndi nkhawa.