Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 37:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Ona munthu wosalakwa ndipo yang’anitsitsa munthu wolungama,+

      Pakuti tsogolo la munthu ameneyu ndi lamtendere.+

  • Miyambo 16:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kupewa zoipa ndiko njira ya anthu owongoka mtima.+ Munthu amene amateteza njira yake, amasunga moyo wake.+

  • Danieli 12:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Anthu ambiri adzadzitsuka,+ adzadziyeretsa+ ndipo adzayengedwa.+ Anthu oipa adzachita zinthu zoipa+ ndipo palibe munthu woipa aliyense amene adzamvetsetse mawu amenewa,+ koma anthu ozindikira adzawamvetsetsa.+

  • 1 Petulo 1:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Tsopano, popeza mwayeretsa+ miyoyo yanu mwa kukhala omvera choonadi ndipo zotsatira zake n’zakuti mumakonda abale mopanda chinyengo,+ kondanani kwambiri kuchokera mumtima.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena