Yobu 29:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Madalitso+ a munthu amene watsala pang’ono kuwonongedwa ankabwera kwa ine,Ndipo ndinkasangalatsa mtima wa mkazi wamasiye.+ Salimo 106:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Odala ndi anthu amene amatsata chilungamo,+Ndi kuchita zolungama nthawi zonse.+
13 Madalitso+ a munthu amene watsala pang’ono kuwonongedwa ankabwera kwa ine,Ndipo ndinkasangalatsa mtima wa mkazi wamasiye.+