Miyambo 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kukhala ndi mkate wouma pali bata,+ kuli bwino kuposa nyumba yodzaza ndi nyama yansembe pali mkangano.+ Miyambo 27:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Denga lodontha limene limathawitsa munthu pa tsiku la mvula yosalekeza, limafanana ndi mkazi wolongolola.+
17 Kukhala ndi mkate wouma pali bata,+ kuli bwino kuposa nyumba yodzaza ndi nyama yansembe pali mkangano.+
15 Denga lodontha limene limathawitsa munthu pa tsiku la mvula yosalekeza, limafanana ndi mkazi wolongolola.+