Miyambo 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwana wopusa amabweretsa mavuto kwa bambo ake,+ ndipo mkazi wolongolola ali ngati denga* lodontha limene limathawitsa munthu.+ Miyambo 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuli bwino kukhala pakona ya denga la nyumba,+ kusiyana ndi kukhala m’nyumba limodzi ndi mkazi wolongolola.+
13 Mwana wopusa amabweretsa mavuto kwa bambo ake,+ ndipo mkazi wolongolola ali ngati denga* lodontha limene limathawitsa munthu.+
9 Kuli bwino kukhala pakona ya denga la nyumba,+ kusiyana ndi kukhala m’nyumba limodzi ndi mkazi wolongolola.+