Miyambo 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuli bwino kukhala pakona ya denga la nyumba,+ kusiyana ndi kukhala m’nyumba limodzi ndi mkazi wolongolola.+ Miyambo 25:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kuli bwino kukhala pakona ya denga la nyumba, kusiyana ndi kukhala m’nyumba limodzi ndi mkazi wolongolola.+ Miyambo 27:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Denga lodontha limene limathawitsa munthu pa tsiku la mvula yosalekeza, limafanana ndi mkazi wolongolola.+
9 Kuli bwino kukhala pakona ya denga la nyumba,+ kusiyana ndi kukhala m’nyumba limodzi ndi mkazi wolongolola.+
24 Kuli bwino kukhala pakona ya denga la nyumba, kusiyana ndi kukhala m’nyumba limodzi ndi mkazi wolongolola.+
15 Denga lodontha limene limathawitsa munthu pa tsiku la mvula yosalekeza, limafanana ndi mkazi wolongolola.+