Miyambo 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kukhala ndi mkate wouma pali bata,+ kuli bwino kuposa nyumba yodzaza ndi nyama yansembe pali mkangano.+ Miyambo 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwana wopusa amabweretsa mavuto kwa bambo ake,+ ndipo mkazi wolongolola ali ngati denga* lodontha limene limathawitsa munthu.+ Miyambo 27:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Denga lodontha limene limathawitsa munthu pa tsiku la mvula yosalekeza, limafanana ndi mkazi wolongolola.+
17 Kukhala ndi mkate wouma pali bata,+ kuli bwino kuposa nyumba yodzaza ndi nyama yansembe pali mkangano.+
13 Mwana wopusa amabweretsa mavuto kwa bambo ake,+ ndipo mkazi wolongolola ali ngati denga* lodontha limene limathawitsa munthu.+
15 Denga lodontha limene limathawitsa munthu pa tsiku la mvula yosalekeza, limafanana ndi mkazi wolongolola.+