2 Samueli 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho anamangira Abisalomu hema padenga,+ ndipo Abisalomu anayamba kugona ndi adzakazi a bambo ake,+ Aisiraeli onse akuona.+ Miyambo 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Miyambi ya Solomo.+ Mwana wanzeru amakondweretsa bambo ake,+ koma mwana wopusa amamvetsa chisoni mayi ake.+ Miyambo 17:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Bambo wa mwana wopusa amamva chisoni,+ ndipo bambo wa mwana wopanda nzeru sasangalala.+
22 Choncho anamangira Abisalomu hema padenga,+ ndipo Abisalomu anayamba kugona ndi adzakazi a bambo ake,+ Aisiraeli onse akuona.+
10 Miyambi ya Solomo.+ Mwana wanzeru amakondweretsa bambo ake,+ koma mwana wopusa amamvetsa chisoni mayi ake.+