Miyambo 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwana wopusa amabweretsa mavuto kwa bambo ake,+ ndipo mkazi wolongolola ali ngati denga* lodontha limene limathawitsa munthu.+ Miyambo 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kuli bwino kukhala m’chipululu kusiyana ndi kukhala mokhumudwa ndi mkazi wolongolola.+ Miyambo 27:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Denga lodontha limene limathawitsa munthu pa tsiku la mvula yosalekeza, limafanana ndi mkazi wolongolola.+
13 Mwana wopusa amabweretsa mavuto kwa bambo ake,+ ndipo mkazi wolongolola ali ngati denga* lodontha limene limathawitsa munthu.+
15 Denga lodontha limene limathawitsa munthu pa tsiku la mvula yosalekeza, limafanana ndi mkazi wolongolola.+