Luka 2:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Koma Yesu anali kukulabe m’nzeru+ ndi mu msinkhu. Ndipo Mulungu ndi anthu anapitiriza kukondwera naye.+ 2 Akorinto 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti “timasamalira zinthu zonse moona mtima, osati pamaso pa Yehova pokha ayi, komanso pamaso pa anthu.”+
52 Koma Yesu anali kukulabe m’nzeru+ ndi mu msinkhu. Ndipo Mulungu ndi anthu anapitiriza kukondwera naye.+
21 Pakuti “timasamalira zinthu zonse moona mtima, osati pamaso pa Yehova pokha ayi, komanso pamaso pa anthu.”+