Salimo 104:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ntchito zanu ndi zochuluka, inu Yehova!+Zonsezo munazipanga mwanzeru zanu.+Dziko lapansi ladzaza ndi zinthu zimene munapanga.+ Miyambo 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nzeru yeniyeni+ yamanga nyumba yake.+ Yasema zipilala zake 7. Miyambo 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mkazi amene alidi wanzeru amamanga nyumba yake,+ koma wopusa amaigwetsa ndi manja ake.+
24 Ntchito zanu ndi zochuluka, inu Yehova!+Zonsezo munazipanga mwanzeru zanu.+Dziko lapansi ladzaza ndi zinthu zimene munapanga.+