Miyambo 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nzeru yeniyeni+ imangokhalira kufuula mumsewu.+ Imangokhalira kutulutsa mawu ake m’mabwalo a mzinda.+ 1 Akorinto 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma tikulankhula za nzeru ya Mulungu imene inaonekera m’chinsinsi chopatulika,+ nzeru yobisika. Mulungu anakonzeratu zochita zimenezi kusanakhale nthawi* zosiyanasiyana,+ kuti tikhale ndi ulemerero.
20 Nzeru yeniyeni+ imangokhalira kufuula mumsewu.+ Imangokhalira kutulutsa mawu ake m’mabwalo a mzinda.+
7 Koma tikulankhula za nzeru ya Mulungu imene inaonekera m’chinsinsi chopatulika,+ nzeru yobisika. Mulungu anakonzeratu zochita zimenezi kusanakhale nthawi* zosiyanasiyana,+ kuti tikhale ndi ulemerero.