33 Ndithudi, madalitso amene Mulungu amapereka ndi ochuluka kwambiri.+ Nzeru+ zake n’zozama, ndiponso iye ndi wodziwa zinthu kwambiri.+ Ziweruzo zake ndi zosasanthulika,+ ndipo ndani angatulukire njira zake?
10 Zinakhala choncho kuti maboma ndi maulamuliro+ amene ali m’malo akumwamba adziwe tsopano mbali zambirimbiri za nzeru ya Mulungu+ kudzera mwa mpingo.+