Aheberi 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndithudi, ganizirani mozama za munthu amene anapirira malankhulidwe onyoza+ ngati amenewo a anthu ochimwa, amene mwa kulankhula koteroko anali kungodzivulaza okha. Ganizirani za munthu ameneyu kuti musatope ndiponso kuti musalefuke.+
3 Ndithudi, ganizirani mozama za munthu amene anapirira malankhulidwe onyoza+ ngati amenewo a anthu ochimwa, amene mwa kulankhula koteroko anali kungodzivulaza okha. Ganizirani za munthu ameneyu kuti musatope ndiponso kuti musalefuke.+