1 Atesalonika 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipotu, sitinayambe talankhulapo mawu okuyamikirani mwachinyengo,+ (monga mukudziwira), kapena kuchita zachiphamaso+ chifukwa cha kusirira kwa nsanje.+ Mulungu ndiye mboni yathu.
5 Ndipotu, sitinayambe talankhulapo mawu okuyamikirani mwachinyengo,+ (monga mukudziwira), kapena kuchita zachiphamaso+ chifukwa cha kusirira kwa nsanje.+ Mulungu ndiye mboni yathu.