Salimo 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino,+Ngati siliva woyengedwa nthawi zokwanira 7 mung’anjo ya m’nthaka. Salimo 66:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti inu Mulungu mwatisanthula,+Mwatiyenga ngati siliva.+
6 Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino,+Ngati siliva woyengedwa nthawi zokwanira 7 mung’anjo ya m’nthaka.