Miyambo 11:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zipatso za munthu wolungama ndizo mtengo wa moyo,+ ndipo munthu wopulumutsa miyoyo ndi wanzeru.+